Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako utenge mafuta odzozera+ ndi kuwathira pamutu pake ndi kum’dzoza.+

  • Ekisodo 30:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Udzoze Aroni+ ndi ana ake,+ ndipo uwayeretse kuti atumikire monga ansembe anga.+

  • Ekisodo 40:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ukatero, udzaveke Aroni zovala zopatulika,+ kenako um’dzoze+ ndi kumuyeretsa kuti atumikire monga wansembe wanga.

  • Levitiko 21:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “‘Ndipo mkulu wa ansembe wokhala pakati pa abale ake ansembe, wodzozedwa mafuta pamutu pake,+ ndi kupatsidwa mphamvu* kuti avale zovala zaunsembe,+ asalekerere tsitsi lake osalisamala+ ndipo asang’ambe zovala zake.+

  • Salimo 133:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Zili ngati mafuta abwino amene athiridwa pamutu,+

      Amene akutsikira kundevu,

      Ndevu za Aroni,+

      Amenenso akuyenderera mpaka m’khosi la zovala zake.+

  • Machitidwe 10:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Nkhani yake inali yonena za Yesu wa ku Nazareti, kuti Mulungu anamudzoza ndi mzimu woyera+ ndi mphamvu. Ndiponso kuti popeza Mulungu anali naye,+ anayendayenda m’dziko, n’kumachita zabwino ndi kuchiritsa onse osautsidwa ndi Mdyerekezi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena