Salimo 45:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zovala zako zonse ndi zonunkhira mafuta a mule, aloye ndi kasiya.*+Umasangalala ndi nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo za zingwe, kuchokera m’chinyumba chachikulu cha mfumu, chokongoletsedwa ndi minyanga ya njovu.+ Nyimbo ya Solomo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wachikondi wanga ali ngati kathumba ka mule*+ kwa ine. Iye adzakhala pakati pa mabere anga+ usiku wonse. Nyimbo ya Solomo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Kodi chinthu chikuchokera kuchipululuchi n’chiyani, chooneka ngati utsi wokwera m’mwamba, chonunkhira mafuta a mule, lubani,*+ ndi mtundu uliwonse wa zonunkhira za ufa za munthu wamalonda?”+
8 Zovala zako zonse ndi zonunkhira mafuta a mule, aloye ndi kasiya.*+Umasangalala ndi nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo za zingwe, kuchokera m’chinyumba chachikulu cha mfumu, chokongoletsedwa ndi minyanga ya njovu.+
13 Wachikondi wanga ali ngati kathumba ka mule*+ kwa ine. Iye adzakhala pakati pa mabere anga+ usiku wonse.
6 “Kodi chinthu chikuchokera kuchipululuchi n’chiyani, chooneka ngati utsi wokwera m’mwamba, chonunkhira mafuta a mule, lubani,*+ ndi mtundu uliwonse wa zonunkhira za ufa za munthu wamalonda?”+