2 Akaziwa anali ochokera m’mitundu imene Yehova anauza ana a Isiraeli kuti: “Musamapite pakati pawo+ ndipo iwonso asamabwere pakati panu, chifukwa ndithu adzapotoza mitima yanu kuti itsatire milungu yawo.”+ Amenewa ndi amene Solomo anaumirira+ kuwakonda.