Ekisodo 31:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 zovala zosokedwa bwino ndi zovala zopatulika za Aroni wansembe, zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe,+ Ekisodo 39:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 zovala+ zosokedwa bwino zoti azivala potumikira m’malo opatulika, zovala zopatulika+ za Aroni wansembe ndi zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe.+
10 zovala zosokedwa bwino ndi zovala zopatulika za Aroni wansembe, zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe,+
41 zovala+ zosokedwa bwino zoti azivala potumikira m’malo opatulika, zovala zopatulika+ za Aroni wansembe ndi zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe.+