Salimo 78:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anapitiriza kuwatsogolera ndi mtambo masana,+Ndipo usiku wonse anali kuwatsogolera ndi kuwala kwa moto.+
14 Iye anapitiriza kuwatsogolera ndi mtambo masana,+Ndipo usiku wonse anali kuwatsogolera ndi kuwala kwa moto.+