Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 11:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno Mose anadandaulira Yehova kuti: “N’chifukwa chiyani mwandivutitsa chonchi ine mtumiki wanu? N’chifukwa chiyani mwandiumira mtima chotere, n’kundisenzetsa chimtolo cha anthu onsewa?+

  • 1 Samueli 30:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Zimenezi zinam’vutitsa maganizo kwambiri Davide+ chifukwanso anthu anali kukambirana zom’ponya miyala.+ Anthuwo anali kukambirana zimenezi chifukwa aliyense wa iwo anali wokwiya kwambiri+ poona zimene zachitikira ana awo aamuna ndi ana awo aakazi. Choncho, Davide anadzilimbitsa mwa Yehova Mulungu wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena