Ekisodo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Mulungu anati: “Chifukwa ndidzakhala nawe.+ Ndipo chizindikiro chako chakuti ine ndi amene ndakutuma ndi ichi:+ Pambuyo powatulutsa anthuwo mu Iguputo, anthu inu mudzatumikira Mulungu woona paphiri lino.”+ Ekisodo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Mose ndi Aroni anapita kwa Farao ndi kumuuza kuti:+ “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Lolani anthu anga apite m’chipululu kuti akachite chikondwerero.’”+
12 Pamenepo Mulungu anati: “Chifukwa ndidzakhala nawe.+ Ndipo chizindikiro chako chakuti ine ndi amene ndakutuma ndi ichi:+ Pambuyo powatulutsa anthuwo mu Iguputo, anthu inu mudzatumikira Mulungu woona paphiri lino.”+
5 Kenako Mose ndi Aroni anapita kwa Farao ndi kumuuza kuti:+ “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Lolani anthu anga apite m’chipululu kuti akachite chikondwerero.’”+