Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 20:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tsopano bweza mkaziyo kwa mwamuna wake. Mwamunayo ndi mneneri,+ ndipo adzakupempherera.+ Ukatero udzakhala ndi moyo. Koma ukapanda kumubweza, udziwe kuti, iweyo ndi anthu ako onse mufa ndithu.”+

  • Ekisodo 10:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chotero ndikhululukireni+ tchimo langa kamodzi kokha kano, ndipo chondererani+ Yehova Mulungu wanu kuti andichotsere mliri wakuphawu.”

  • Numeri 21:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anthuwo ataona zimenezo, anapita kwa Mose n’kumuuza kuti: “Tachimwa ife,+ chifukwa talankhula mowiringula kwa Yehova ndiponso kwa inuyo. Tipepesereni kwa Yehova kuti atichotsere njokazi.”+ Pamenepo Mose anayamba kuwapepesera kwa Mulungu.+

  • 1 Mafumu 13:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano mfumuyo inauza munthu wa Mulungu woonayo kuti: “Chonde! Khazikani pansi mtima wa Yehova Mulungu wanu. Mundipempherere kuti dzanja langa libwerere mwakale.”+ Choncho munthu wa Mulungu woona uja anakhazikadi pansi+ mtima wa Yehova, moti dzanja la mfumu linabwerera mwakale, n’kukhala ngati mmene linalili poyamba.+

  • Machitidwe 8:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Poyankha Simoni uja anati: “Amuna inu, ndipemphereni chonde kwa Yehova mopembedzera+ kuti zonse mwanenazo zisandigwere.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena