Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 8:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Farao ataona kuti mliri wa achulewo watha, anaumitsa mtima wake,+ ndipo sanamvere Mose ndi Aroni, monga momwe Yehova ananenera.+

  • Ekisodo 8:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Pamenepo Mose anati: “Mmene ndikuchoka pano, ndikukachonderera Yehova ndipo mawa tizilomboti tichoka pa Farao, atumiki ake ndi anthu ake. Koma Farao asatipusitsenso mwa kusalola anthu kupita kuti akapereke nsembe kwa Yehova.”+

  • Ekisodo 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Zitatero anabweretsanso Mose ndi Aroni kwa Farao ndipo iye anati: “Pitani, katumikireni Yehova Mulungu wanu.+ Ndani kwenikweni amene akupita?”

  • Ekisodo 12:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Nthawi yomweyo Farao anaitanitsa+ Mose ndi Aroni usiku, ndipo anati: “Nyamukani, chokani pakati pa anthu anga, inuyo ndi ana onse a Isiraeli. Pitani, katumikireni Yehova, monga momwe mwanenera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena