Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 3:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndidzatambasula dzanja langa+ ndi kukantha Iguputo ndi ntchito zanga zonse zodabwitsa zimene ndidzazichita m’dzikolo. Pamenepo adzakulolani kuchoka.+

  • Ekisodo 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Tsopano uona zimene ndichite kwa Farao.+ Chifukwa cha dzanja lamphamvu, iye awalola kuchoka, ndipo chifukwa cha dzanja lamphamvu awatulutsa m’dziko lake.”+

  • Ekisodo 10:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamenepo Mose anati: “Tipita ndi achinyamata athu ndi achikulire omwe. Tipita ndi ana athu aamuna ndi ana athu aakazi+ pamodzi ndi nkhosa ndi ng’ombe zathu,+ chifukwa tikukachitira Yehova chikondwerero.”+

  • Salimo 105:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Aiguputo anasangalala pamene Aisiraeli anatuluka m’dzikolo,

      Pakuti anali kuwaopa kwambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena