Ekisodo 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Achulewo adzachuluka kwambiri mumtsinje wa Nailo, ndipo adzatuluka mumtsinjemo ndi kulowa m’nyumba yako, m’chipinda chako chogona, pabedi pako, ndiponso m’nyumba za atumiki ako, za anthu ako, m’mauvuni ako, ndi m’ziwiya zako zokandiramo ufa.+
3 Achulewo adzachuluka kwambiri mumtsinje wa Nailo, ndipo adzatuluka mumtsinjemo ndi kulowa m’nyumba yako, m’chipinda chako chogona, pabedi pako, ndiponso m’nyumba za atumiki ako, za anthu ako, m’mauvuni ako, ndi m’ziwiya zako zokandiramo ufa.+