Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 43:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Iwo anaikira Yosefe chakudya payekha. Abale akewo anawaikiranso paokha. Nawonso Aiguputo amene ankadya m’nyumba mwake anawaikira paokha. Aiguputo sankadya limodzi ndi Aheberi, chifukwa chinali chinthu chonyansa kwa iwo.+

  • Genesis 46:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Inu mukayankhe kuti: ‘Akapolo anufe takhala tikuweta ziweto kuyambira tili ana kufikira lero, ifeyo ndi makolo athu omwe.’+ Mukayankhe choncho kuti mukhale ku Goseni,+ chifukwa aliyense woweta nkhosa Aiguputo amanyansidwa naye.”+

  • Ekisodo 10:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Komanso ziweto zathu tipita nazo.+ Sitidzasiya chiweto ngakhale chimodzi, chifukwa tiyenera kukatengapo zina ndi kukazigwiritsa ntchito polambira Yehova Mulungu wathu.+ Pakali pano sitikudziwa kuti tikapereka chiyani polambira Yehova mpaka titakafika kumeneko.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena