Ekisodo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Mose ndi Aroni anapita kwa Farao ndi kumuuza kuti:+ “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Lolani anthu anga apite m’chipululu kuti akachite chikondwerero.’”+ Ekisodo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa Farao, ukamuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Lola anthu anga apite kuti akanditumikire.+
5 Kenako Mose ndi Aroni anapita kwa Farao ndi kumuuza kuti:+ “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Lolani anthu anga apite m’chipululu kuti akachite chikondwerero.’”+
8 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa Farao, ukamuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Lola anthu anga apite kuti akanditumikire.+