Ekisodo 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Taona, mawa pa nthawi ngati ino ndigwetsa mvula yamphamvu kwambiri ya matalala, matalala amene sanayambe agwapo mu Iguputo m’mbiri yake yonse mpaka lero.+
18 Taona, mawa pa nthawi ngati ino ndigwetsa mvula yamphamvu kwambiri ya matalala, matalala amene sanayambe agwapo mu Iguputo m’mbiri yake yonse mpaka lero.+