Yesaya 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kodi iye akasalaza dothilo si paja amawazapo chitowe chakuda ndiponso amafesapo chitowe chamtundu wina?+ Kodi si paja amabzalanso tirigu, mapira+ ndi balere m’malo ake,+ ndipo m’mphepete mwa mundawo+ amabzalamo mbewu zinanso?*+ Ezekieli 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Tenga tirigu,+ balere, nyemba zikuluzikulu,+ mphodza,+ mapira, ndi tirigu wamtundu wina.*+ Zonsezo uziike mumphika umodzi kuti zikhale chakudya chako cha masiku amene udzakhale ukugonera mbali imodzi. Udzadye chakudya chimenechi kwa masiku 390.+
25 Kodi iye akasalaza dothilo si paja amawazapo chitowe chakuda ndiponso amafesapo chitowe chamtundu wina?+ Kodi si paja amabzalanso tirigu, mapira+ ndi balere m’malo ake,+ ndipo m’mphepete mwa mundawo+ amabzalamo mbewu zinanso?*+
9 “Tenga tirigu,+ balere, nyemba zikuluzikulu,+ mphodza,+ mapira, ndi tirigu wamtundu wina.*+ Zonsezo uziike mumphika umodzi kuti zikhale chakudya chako cha masiku amene udzakhale ukugonera mbali imodzi. Udzadye chakudya chimenechi kwa masiku 390.+