Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 13:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chotero Mose anauza anthuwo kuti: “Muzikumbukira tsiku lino limene munatuluka mu Iguputo,+ m’nyumba ya ukapolo, chifukwa Yehova anakutulutsani mmenemo ndi mphamvu ya dzanja lake.+ Choncho musadye chilichonse chokhala ndi chofufumitsa.+

  • Ekisodo 34:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “Popereka magazi a nsembe yanga musawapereke limodzi ndi chilichonse chofufumitsa.+ Ndipo nsembe ya chikondwerero cha pasika isamagone mpaka m’mawa.+

  • Deuteronomo 16:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Usadye nsembeyo pamodzi ndi chilichonse chokhala ndi chofufumitsa. Masiku 7+ uzidya mkate wopanda chofufumitsa, umene ndi mkate wa nsautso, chifukwa unatuluka mofulumira m’dziko la Iguputo.+ Uzichita zimenezi kuti uzikumbukira tsiku limene unatuluka m’dziko la Iguputo, masiku onse a moyo wako.+

  • 1 Akorinto 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chotero tiyeni tichite chikondwererochi,+ osati ndi chofufumitsa chakale,+ kapena chofufumitsa+ choimira zoipa ndi uchimo,+ koma ndi mikate yopanda chofufumitsa yoimira kuona mtima ndi choonadi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena