Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 15:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma mtundu umene adzautumikirewo ndidzauweruza.+ Pambuyo pake, iwo adzachokako ndi katundu wochuluka.+

  • Numeri 33:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pa nthawiyi n’kuti Aiguputo ali pa ntchito yoika m’manda ana onse oyamba kubadwa,+ amene Yehova anawapha pakati pawo. Yehovayo anali atapereka ziweruzo pamilungu yawo.+

  • Salimo 78:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Pamapeto pake anapha ana onse oyamba kubadwa mu Iguputo,+

      Amene ndi chiyambi cha mphamvu zawo zobereka m’mahema a Hamu.+

  • Salimo 105:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Mulungu anapha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko lawo,+

      Chiyambi cha mphamvu zawo zonse zobereka.+

  • Salimo 136:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Yamikani amene anakantha Aiguputo mwa kupha ana awo oyamba kubadwa:+

      Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+

  • Aheberi 11:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Mwa chikhulupiriro, iye anachita pasika+ ndiponso anawaza magazi pamafelemu a pakhomo,+ kuti wowonongayo asakhudze ana awo oyamba kubadwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena