Ekisodo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Mose ndi Aroni anachitadi monga momwe Yehova anawalamulira.+ Anachitadi momwemo.+ Ekisodo 39:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chotero ntchito yonse ya chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako, inatha, chifukwa ana a Isiraeli anachita zonse monga mmene Yehova analamulira Mose.+ Anachitadi momwemo. Deuteronomo 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Muzichita mosamala mawu onse amene ndikukuuzani.+ Musawonjezepo kapena kuchotsapo kalikonse.+
32 Chotero ntchito yonse ya chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako, inatha, chifukwa ana a Isiraeli anachita zonse monga mmene Yehova analamulira Mose.+ Anachitadi momwemo.