Ekisodo 12:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno ana anu akadzakufunsani kuti, ‘Kodi mwambo umenewu umatanthauza chiyani?’+ Deuteronomo 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Mwana wako akadzakufunsa tsiku lina m’tsogolo+ kuti, ‘Kodi zikumbutso, malangizo ndi zigamulo izi zimene Yehova Mulungu wathu anakupatsani, zimatanthauza chiyani?’ Salimo 145:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu adzatamanda ntchito zanu ku mibadwomibadwo,+Ndipo adzasimba za zochita zanu zamphamvu.+
20 “Mwana wako akadzakufunsa tsiku lina m’tsogolo+ kuti, ‘Kodi zikumbutso, malangizo ndi zigamulo izi zimene Yehova Mulungu wathu anakupatsani, zimatanthauza chiyani?’