Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndiyeno pa nthawi ya ulonda wam’mawa,* Yehova ali mumtambo ndi moto woima njo ngati chipilala,+ anayang’ana gulu la Aiguputo, ndipo anachititsa Aiguputowo kusokonezeka.+

  • Numeri 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iwo akamva adzauza anthu a m’dziko lino, amene amva kuti inu Yehova muli pakati pa anthu anu,+ ndi kuti mumaonekera kwa iwo pamasom’pamaso.+ Inu ndinu Yehova, ndipo mtambo wanu uli pamwamba pawo. Masana mumawatsogolera mumtambo woima njo ngati chipilala, pamene usiku mumawatsogolera m’lawi lamoto.+

  • Salimo 78:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iye anapitiriza kuwatsogolera ndi mtambo masana,+

      Ndipo usiku wonse anali kuwatsogolera ndi kuwala kwa moto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena