Ekisodo 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mahatchi a Farao,+ magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi atalowa m’nyanja,+Yehova wabweza madzi a m’nyanjamo ndi kuwamiza.+Koma ana a Isiraeli ayenda panthaka youma pakati pa nyanja.”+ Numeri 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo pake ananyamuka ku Pihahiroti, n’kukadutsa panyanja+ kuwolokera kuchipululu.+ Anayendabe ulendo wa masiku atatu m’chipululu cha Etamu,+ n’kukamanga msasa ku Mara.+ Yesaya 63:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 amene anawawolotsa pamadzi amphamvu moti sanapunthwe, mofanana ndi hatchi m’chipululu?+ 1 Akorinto 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano sindikufuna kuti mukhale osadziwa abale, kuti makolo athu akale, onse anali pansi pa mtambo+ ndipo onse anawoloka nyanja.+ Aheberi 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mwa chikhulupiriro, anthu a Mulunguwo anawoloka Nyanja Yofiira ngati kuti akudutsa pamtunda pouma,+ koma Aiguputo atalimba mtima ndi kulowa panyanjapo, nyanjayo inawamiza.+
19 Mahatchi a Farao,+ magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi atalowa m’nyanja,+Yehova wabweza madzi a m’nyanjamo ndi kuwamiza.+Koma ana a Isiraeli ayenda panthaka youma pakati pa nyanja.”+
8 Pambuyo pake ananyamuka ku Pihahiroti, n’kukadutsa panyanja+ kuwolokera kuchipululu.+ Anayendabe ulendo wa masiku atatu m’chipululu cha Etamu,+ n’kukamanga msasa ku Mara.+
10 Tsopano sindikufuna kuti mukhale osadziwa abale, kuti makolo athu akale, onse anali pansi pa mtambo+ ndipo onse anawoloka nyanja.+
29 Mwa chikhulupiriro, anthu a Mulunguwo anawoloka Nyanja Yofiira ngati kuti akudutsa pamtunda pouma,+ koma Aiguputo atalimba mtima ndi kulowa panyanjapo, nyanjayo inawamiza.+