Levitiko 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Mukapitiriza kutsatira malangizo anga ndi kusunga malamulo anga,+ Deuteronomo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Ukamveradi mawu a Yehova Mulungu wako mwa kuonetsetsa kuti ukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsa lero,+ Yehova Mulungu wako adzakukweza ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+ 1 Yohane 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+
28 “Ukamveradi mawu a Yehova Mulungu wako mwa kuonetsetsa kuti ukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsa lero,+ Yehova Mulungu wako adzakukweza ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+
3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+