Deuteronomo 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Muzikumbukira zimene Aamaleki anakuchitirani panjira pamene munali kutuluka mu Iguputo.+ 1 Samueli 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wa makamu+ wanena kuti, ‘Ndibwezera+ Aamaleki chifukwa choukira Aisiraeli panjira, pamene Aisiraeliwo anali kutuluka mu Iguputo.+
2 Yehova wa makamu+ wanena kuti, ‘Ndibwezera+ Aamaleki chifukwa choukira Aisiraeli panjira, pamene Aisiraeliwo anali kutuluka mu Iguputo.+