Ekisodo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Aamaleki+ anabwera kudzamenyana ndi Isiraeli ku Refidimu.+ Numeri 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Balamu ataona Amaleki, anapitiriza mawu ake a ndakatulo, kuti:+“Amaleki anali woyamba wa anthu a mitundu ina,+Koma chiwonongeko chake chidzakhaladi mapeto ake.”+
20 Tsopano Balamu ataona Amaleki, anapitiriza mawu ake a ndakatulo, kuti:+“Amaleki anali woyamba wa anthu a mitundu ina,+Koma chiwonongeko chake chidzakhaladi mapeto ake.”+