Yesaya 66:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Yehova wanena kuti: “Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi anthu inu mungandimangire nyumba yotani?+ Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo, ali kuti?”+ Machitidwe 7:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 ‘Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi inu mudzandimangira nyumba yotani? akutero Yehova. Kapena malo oti ine ndipumuliremo ali kuti?+
66 Yehova wanena kuti: “Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi anthu inu mungandimangire nyumba yotani?+ Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo, ali kuti?”+
49 ‘Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi inu mudzandimangira nyumba yotani? akutero Yehova. Kapena malo oti ine ndipumuliremo ali kuti?+