2 Mbiri 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Koma kodi Mulungu angakhaledi ndi anthu padziko lapansi?+ Taonani! Kumwamba, ngakhale kumwambamwamba, simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba imene ndamangayi?+ Machitidwe 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mulungu amene anapanga dzikoli ndi zinthu zonse zili mmenemu, sakhala mu akachisi opangidwa ndi manja.+ Iye ndiye Ambuye wakumwamba ndi dziko lapansi.+
18 “Koma kodi Mulungu angakhaledi ndi anthu padziko lapansi?+ Taonani! Kumwamba, ngakhale kumwambamwamba, simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba imene ndamangayi?+
24 Mulungu amene anapanga dzikoli ndi zinthu zonse zili mmenemu, sakhala mu akachisi opangidwa ndi manja.+ Iye ndiye Ambuye wakumwamba ndi dziko lapansi.+