Numeri 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Mose anadandaulira Yehova kuti: “N’chifukwa chiyani mwandivutitsa chonchi ine mtumiki wanu? N’chifukwa chiyani mwandiumira mtima chotere, n’kundisenzetsa chimtolo cha anthu onsewa?+
11 Ndiyeno Mose anadandaulira Yehova kuti: “N’chifukwa chiyani mwandivutitsa chonchi ine mtumiki wanu? N’chifukwa chiyani mwandiumira mtima chotere, n’kundisenzetsa chimtolo cha anthu onsewa?+