Ekisodo 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Usalandire chiphuphu chifukwa chiphuphu chimachititsa khungu anthu amaso akuthwa, ndipo chingapotoze mawu a anthu olungama.+ Machitidwe 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Sindinasirire mwa nsanje siliva, golide kapena chovala cha munthu.+ 1 Timoteyo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Asakhale munthu womwa mowa mwauchidakwa,*+ kapena wandewu,+ koma wololera.+ Asakhale waukali,+ kapena wokonda ndalama.+ 1 Petulo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Wetani+ gulu la nkhosa za Mulungu+ lomwe analisiya m’manja mwanu, osati mokakamizika, koma mofunitsitsa.+ Osatinso chifukwa chofuna kupindulapo kenakake,+ koma ndi mtima wonse.
8 “Usalandire chiphuphu chifukwa chiphuphu chimachititsa khungu anthu amaso akuthwa, ndipo chingapotoze mawu a anthu olungama.+
3 Asakhale munthu womwa mowa mwauchidakwa,*+ kapena wandewu,+ koma wololera.+ Asakhale waukali,+ kapena wokonda ndalama.+
2 Wetani+ gulu la nkhosa za Mulungu+ lomwe analisiya m’manja mwanu, osati mokakamizika, koma mofunitsitsa.+ Osatinso chifukwa chofuna kupindulapo kenakake,+ koma ndi mtima wonse.