Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 10:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Anaberekanso Ayebusi,+ Aamori,+ Agirigasi,

  • Ekisodo 33:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndipo ndidzatumiza mngelo patsogolo panu+ kuti akathamangitse Akanani, Aamori, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+

  • Deuteronomo 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Yehova Mulungu wako akadzakulowetsa m’dziko limene ukupita kukalitenga kukhala lako,+ adzakuchotsera mitundu ikuluikulu.+ Adzakuchotsera Ahiti,+ Agirigasi,+ Aamori,+ Akanani,+ Aperezi,+ Ahivi+ ndi Ayebusi,+ mitundu 7 ikuluikulu ndi yamphamvu kuposa iwe.+

  • Yoswa 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Atafika, Yoswa anati: “Mukaona zimene zichitike pano, mudziwa kuti Mulungu wamoyo alidi pakati panu.+ Mudziwanso kuti iye adzathamangitsadi pamaso panu Akanani, Ahiti, Ahivi, Aperezi, Agirigasi, Aamori ndi Ayebusi.+

  • Nehemiya 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Munamuona kuti anali ndi mtima wokhulupirika pamaso panu.+ Chotero munachita naye pangano+ kuti mudzam’patsa dziko la Akanani, Ahiti, Aamori, Aperezi, Ayebusi ndi Agirigasi. Munachita naye pangano kuti mudzapereka dziko limeneli kwa mbewu yake,+ ndipo munachitadi zimene munanena chifukwa ndinu wolungama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena