Numeri 30:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Awa ndiwo malangizo amene Yehova anapatsa Mose okhudza mwamuna ndi mkazi wake,+ ndiponso bambo ndi mwana wake wachitsikana amene akukhalabe m’nyumba mwake.”+
16 “Awa ndiwo malangizo amene Yehova anapatsa Mose okhudza mwamuna ndi mkazi wake,+ ndiponso bambo ndi mwana wake wachitsikana amene akukhalabe m’nyumba mwake.”+