Deuteronomo 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Munthu akaba+ mmodzi mwa abale ake, ana a Isiraeli, n’kumuchitira nkhanza ndiponso kum’gulitsa,+ wakuba munthuyo afe ndithu. Muzichotsa woipayo pakati panu.+
7 “Munthu akaba+ mmodzi mwa abale ake, ana a Isiraeli, n’kumuchitira nkhanza ndiponso kum’gulitsa,+ wakuba munthuyo afe ndithu. Muzichotsa woipayo pakati panu.+