Genesis 40:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuti ndipezeke kuno anachita chondiba kudziko la Aheberi,+ ndiponso kuno palibe chilichonse chimene ndinalakwa choti andiikire m’ndende muno.”+ Ekisodo 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Wakuba munthu+ ndi kum’gulitsa+ kapena munthu amene wapezeka ndi munthu wobedwayo, aziphedwa ndithu.+ 1 Timoteyo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 adama,+ amuna ogonana ndi amuna anzawo, oba anthu, onama, olumbira monama,+ ndiponso ochita china chilichonse chosagwirizana+ ndi chiphunzitso cholondola.+
15 Kuti ndipezeke kuno anachita chondiba kudziko la Aheberi,+ ndiponso kuno palibe chilichonse chimene ndinalakwa choti andiikire m’ndende muno.”+
16 “Wakuba munthu+ ndi kum’gulitsa+ kapena munthu amene wapezeka ndi munthu wobedwayo, aziphedwa ndithu.+
10 adama,+ amuna ogonana ndi amuna anzawo, oba anthu, onama, olumbira monama,+ ndiponso ochita china chilichonse chosagwirizana+ ndi chiphunzitso cholondola.+