Levitiko 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Wokantha ndi kupheratu chiweto cha mnzake+ azilipira,+ koma wokantha ndi kupha munthu nayenso aziphedwa.+
21 Wokantha ndi kupheratu chiweto cha mnzake+ azilipira,+ koma wokantha ndi kupha munthu nayenso aziphedwa.+