Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 31:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Chifukwa choopa khamu lalikulu,

      Ndiponso chifukwa choopa kunyozedwa ndi mabanja,

      Ndinkakhala chete, sindinkatuluka pakhomo.

  • Luka 23:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Atamva izi, anayamba kumuumiriza mokweza mawu, ndi kumupempha kuti Yesu apachikidwe basi. Anthuwo anali kufuula mwamphamvu moti Pilato anangololera.+

  • Machitidwe 25:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma pofuna kuti Ayudawo amukonde,+ Fesito anayankha Paulo kuti: “Kodi ukufuna kupita ku Yerusalemu, kuti nkhani imeneyi ikaweruzidwe kumeneko pamaso panga?”+

  • Aroma 1:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Amenewa ngakhale kuti amalidziwa bwino lamulo lolungama la Mulungu,+ lakuti amene amachita zinthu zimenezi n’ngoyenera imfa,+ iwo amapitiriza kuzichita. Kuwonjezera apo, amagwirizananso+ ndi anthu amene amachita zimenezo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena