Levitiko 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Musabe,+ musanamizane+ ndipo aliyense asachitire mnzake chinyengo.+ Luka 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso, asilikali anali kumufunsa kuti: “Nanga ife tichite chiyani?” Iye anali kuwauza kuti: “Musamavutitse anthu kapena kunamizira+ aliyense, koma muzikhutira ndi zimene mumalandira.”+ Aefeso 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+
14 Komanso, asilikali anali kumufunsa kuti: “Nanga ife tichite chiyani?” Iye anali kuwauza kuti: “Musamavutitse anthu kapena kunamizira+ aliyense, koma muzikhutira ndi zimene mumalandira.”+
25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+