Ekisodo 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Usafalitse nkhani yabodza.+ Usagwirizane ndi munthu woipa mwa kukhala mboni yokonzera wina zoipa.+ Ekisodo 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Utalikirane ndi mawu onama.+ Usaphe munthu wosalakwa ndi munthu wolungama, chifukwa woipa sindidzamuyesa wolungama.+ Levitiko 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Musabe,+ musanamizane+ ndipo aliyense asachitire mnzake chinyengo.+ Miyambo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 mboni yachinyengo yonena mabodza,+ ndi aliyense woyambitsa mikangano pakati pa abale.+
23 “Usafalitse nkhani yabodza.+ Usagwirizane ndi munthu woipa mwa kukhala mboni yokonzera wina zoipa.+
7 “Utalikirane ndi mawu onama.+ Usaphe munthu wosalakwa ndi munthu wolungama, chifukwa woipa sindidzamuyesa wolungama.+