Ekisodo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero ndidzakutengani kukhala anthu anga,+ ndi kukusonyezani kuti ndine Mulungu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndidzakutulutsani mu Iguputo, ndi kukuchotserani goli lawo.+ Numeri 15:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo, kuti ndionetse kuti ndine Mulungu wanu.+ Ndine Yehova Mulungu wanu.’”+
7 Chotero ndidzakutengani kukhala anthu anga,+ ndi kukusonyezani kuti ndine Mulungu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndidzakutulutsani mu Iguputo, ndi kukuchotserani goli lawo.+
41 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo, kuti ndionetse kuti ndine Mulungu wanu.+ Ndine Yehova Mulungu wanu.’”+