Genesis 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dziko limene ukukhalamo ngati mlendoli,+ ndidzalipereka kwa iwe ndi mbewu yako yobwera pambuyo pako. Dziko lonse la Kanani lidzakhala lawo mpaka kalekale, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”+ Ekisodo 29:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Choncho ndidzakhala pakati pa ana a Isiraeli, ndipo ndidzakhala Mulungu wawo.+ Levitiko 25:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ine ndine Yehova Mulungu wanu amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo, kuti ndikupatseni dziko la Kanani.+ Ndinachita izi kuti ndikusonyezeni kuti ine ndine Mulungu wanu.+
8 Dziko limene ukukhalamo ngati mlendoli,+ ndidzalipereka kwa iwe ndi mbewu yako yobwera pambuyo pako. Dziko lonse la Kanani lidzakhala lawo mpaka kalekale, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”+
38 Ine ndine Yehova Mulungu wanu amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo, kuti ndikupatseni dziko la Kanani.+ Ndinachita izi kuti ndikusonyezeni kuti ine ndine Mulungu wanu.+