Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 5:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndiyeno chifukwa choti wachimwira malo oyera azilipira mwa kubweza zinthu zopatulikazo ndiponso aziwonjezerapo limodzi mwa magawo asanu+ a malipirowo. Malipirowo aziwapereka kwa wansembe, ndipo mwa kupereka nkhosa ya nsembe ya kupalamula, wansembeyo aziphimba machimo+ a munthuyo ndipo azikhululukidwa.+

  • Levitiko 6:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 kapena chilichonse chimene angalumbirire monama. Azibweza+ chinthucho ndi kuwonjezerapo limodzi mwa magawo ake asanu. Iye azibweza zimenezi kwa mwiniwake, tsiku limene kulakwa kwake kwatsimikizidwa.

  • Levitiko 22:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Munthu akadya mosadziwa chinthu chopatulika,+ azibwezera chinthucho ndi kuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo ake asanu.+ Azipereka chinthu chopatulikacho kwa wansembe.

  • Levitiko 27:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma ngati wopereka mundayo angauwombole, azipereka mtengo wake woikidwiratu ndi kuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo ake asanu, akatero mundawo uzikhaladi wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena