Levitiko 14:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 wansembe azituluka m’nyumbamo n’kukaima pakhomo, ndipo azitseka+ nyumbayo masiku 7. Numeri 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero Miriamu anatulutsidwa kukakhala kunja kwa msasa masiku 7,+ ndipo anthuwo sanasamuke kufikira Miriamu atalandiridwanso mumsasa.
15 Chotero Miriamu anatulutsidwa kukakhala kunja kwa msasa masiku 7,+ ndipo anthuwo sanasamuke kufikira Miriamu atalandiridwanso mumsasa.