Deuteronomo 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Yehova adzakulanga ndi zithupsa za ku Iguputo,+ matenda a mudzi,* ziwengo ndi zotupa, ndipo sudzachira matenda amenewa. 2 Mafumu 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Yesaya anati: “Amuna inu, tengani nkhuyu zouma zoumba pamodzi.”+ Choncho iwo anatenga nkhuyuzo n’kuziika pachithupsa+ chimene anali nacho, ndipo Hezekiya anachira pang’onopang’ono.+ Yobu 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Satana anachoka pamaso pa Yehova+ n’kukagwetsera Yobu zilonda zopweteka,+ kuyambira kuphazi mpaka kumutu.
27 “Yehova adzakulanga ndi zithupsa za ku Iguputo,+ matenda a mudzi,* ziwengo ndi zotupa, ndipo sudzachira matenda amenewa.
7 Kenako Yesaya anati: “Amuna inu, tengani nkhuyu zouma zoumba pamodzi.”+ Choncho iwo anatenga nkhuyuzo n’kuziika pachithupsa+ chimene anali nacho, ndipo Hezekiya anachira pang’onopang’ono.+
7 Kenako Satana anachoka pamaso pa Yehova+ n’kukagwetsera Yobu zilonda zopweteka,+ kuyambira kuphazi mpaka kumutu.