Levitiko 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno wansembe azionanso munthuyo pa tsiku la 7, ndipo ngati nthendayo yaoneka kuti yatha, moti sinafalikire pakhungu, wansembe azibindikiritsa+ munthuyo masiku enanso 7. Numeri 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lamula ana a Isiraeli kuti azitulutsa mumsasa munthu aliyense wakhate,+ aliyense wakukha kumaliseche,+ ndi aliyense wodetsedwa chifukwa chokhudza mtembo wa munthu.+ Numeri 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero Miriamu anatulutsidwa kukakhala kunja kwa msasa masiku 7,+ ndipo anthuwo sanasamuke kufikira Miriamu atalandiridwanso mumsasa.
5 Ndiyeno wansembe azionanso munthuyo pa tsiku la 7, ndipo ngati nthendayo yaoneka kuti yatha, moti sinafalikire pakhungu, wansembe azibindikiritsa+ munthuyo masiku enanso 7.
2 “Lamula ana a Isiraeli kuti azitulutsa mumsasa munthu aliyense wakhate,+ aliyense wakukha kumaliseche,+ ndi aliyense wodetsedwa chifukwa chokhudza mtembo wa munthu.+
15 Chotero Miriamu anatulutsidwa kukakhala kunja kwa msasa masiku 7,+ ndipo anthuwo sanasamuke kufikira Miriamu atalandiridwanso mumsasa.