Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 14:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pa tsiku la 7 azimeta tsitsi lake lonse lakumutu,+ ndevu zake zonse ndi nsidze zonse. Azimeta tsitsi lake lonse, ndipo azichapa zovala zake ndi kusamba madzi otunga kumtsinje. Akatero, azikhala woyera.

  • Numeri 19:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Munthu woteroyo azidziyeretsa ndi madzi oyeretsera aja pa tsiku lachitatu,+ ndipo pa tsiku la 7 azikhala woyera. Koma akapanda kudziyeretsa pa tsiku lachitatu, sadzakhala woyera pa tsiku la 7.

  • Numeri 31:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mumange msasa kunja kwa msasawu, ndipo mukhalemo masiku 7. Aliyense amene wapha munthu,+ ndi aliyense amene wakhudza mtembo wa munthu wophedwa,+ nonsenu, mudziyeretse+ pa tsiku lachitatu ndi pa tsiku la 7. Mudziyeretse limodzinso ndi anthu amene mwawagwirawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena