Ekisodo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aroni m’bale wako umupangire zovala zopatulika kuti zimupatse ulemerero ndi kum’kongoletsa.+ Ekisodo 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Zovala zopatulika+ za Aroni zidzakhala za ana ake+ obwera m’mbuyo mwake. Adzawadzoza+ ndi kuwapatsa mphamvu atavala zovala zimenezi.+ Aheberi 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiponso, panayenera kukhala ansembe ambiri olowana m’malo+ chifukwa imfa+ inali kuwaletsa kupitiriza unsembe wawo.
29 “Zovala zopatulika+ za Aroni zidzakhala za ana ake+ obwera m’mbuyo mwake. Adzawadzoza+ ndi kuwapatsa mphamvu atavala zovala zimenezi.+
23 Ndiponso, panayenera kukhala ansembe ambiri olowana m’malo+ chifukwa imfa+ inali kuwaletsa kupitiriza unsembe wawo.