Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Munthu ameneyo adzakhala ngati mtengo wobzalidwa m’mphepete mwa mitsinje ya madzi,+

      Umene umabala zipatso m’nyengo yake,+

      Umenenso masamba ake safota,+

      Ndipo zochita zake zonse zidzamuyendera bwino.+

  • Salimo 92:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Wolungama adzakula ngati mtengo wa kanjedza,+

      Ndipo adzakula kwambiri ngati mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni.+

  • Yeremiya 17:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Adzakhala ngati mtengo wobzalidwa m’mphepete mwa madzi, umene mizu yake imakafika m’ngalande za madzi. Kutentha kukadzafika iye sadzadziwa, koma masamba ake adzachuluka ndi kukhala obiriwira.+ Pa nthawi ya chilala+ sadzada nkhawa kapena kusiya kubala zipatso.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena