Ekisodo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo ana aamuna a Merari anali Mali ndi Musi.+ Amenewa ndiwo anali mabanja a Alevi malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+ Numeri 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Uwerenge ana a Levi potsata nyumba ya makolo awo, malinga ndi mabanja awo. Uwerenge mwamuna aliyense kuyambira wamwezi umodzi kupita m’tsogolo.”+ Yoswa 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Alevi alibe gawo pakati panu,+ chifukwa cholowa chawo ndi unsembe wa Yehova.+ Fuko la Gadi, Rubeni,+ ndi hafu ya fuko la Manase+ analandira kale cholowa chawo, chimene Mose mtumiki wa Yehova anawapatsa kutsidya la kum’mawa la Yorodano.”+
19 Ndipo ana aamuna a Merari anali Mali ndi Musi.+ Amenewa ndiwo anali mabanja a Alevi malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+
15 “Uwerenge ana a Levi potsata nyumba ya makolo awo, malinga ndi mabanja awo. Uwerenge mwamuna aliyense kuyambira wamwezi umodzi kupita m’tsogolo.”+
7 Alevi alibe gawo pakati panu,+ chifukwa cholowa chawo ndi unsembe wa Yehova.+ Fuko la Gadi, Rubeni,+ ndi hafu ya fuko la Manase+ analandira kale cholowa chawo, chimene Mose mtumiki wa Yehova anawapatsa kutsidya la kum’mawa la Yorodano.”+