Yoswa 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ana a Merari+ anapatsidwa mizinda 12 yochokera m’fuko la Rubeni,+ Gadi,+ ndi Zebuloni,+ potsata mabanja awo. 1 Mbiri 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ana a Levi+ anali Gerisoni,+ Kohati,+ ndi Merari.+
7 Ana a Merari+ anapatsidwa mizinda 12 yochokera m’fuko la Rubeni,+ Gadi,+ ndi Zebuloni,+ potsata mabanja awo.