Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Chakhumi chimene ana a Isiraeli azipereka kwa Yehova monga chopereka, ndawapatsa Alevi monga cholowa chawo. N’chifukwa chake ndinawauza kuti, ‘Asalandire cholowa pakati pa ana a Isiraeli.’”+

  • Deuteronomo 10:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 N’chifukwa chake Levi alibe gawo ndiponso cholowa+ monga abale ake. Yehova ndiye cholowa chake, monga mmene Yehova Mulungu wanu anamuuzira.+

  • Deuteronomo 14:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Mlevi wokhala mumzinda wanu usamutaye,+ pakuti alibe gawo kapena cholowa monga iwe.+

  • Yoswa 14:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mose anali atagawira kale cholowa mafuko awiri ndi hafu kutsidya lina la Yorodano.+ Koma Alevi sanawapatse cholowa pakati pawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena