1 Samueli 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo Ahimeleki anafunsira+ kwa Yehova m’malo mwa Davide, kenako anam’patsa chakudya+ ndi lupanga+ la Goliyati Mfilisiti.” 1 Samueli 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngakhale kuti anali kufunsira kwa Yehova,+ Yehova sanamuyankhe+ kaya kudzera m’maloto,+ Urimu+ kapena kudzera mwa aneneri.+
10 Ndipo Ahimeleki anafunsira+ kwa Yehova m’malo mwa Davide, kenako anam’patsa chakudya+ ndi lupanga+ la Goliyati Mfilisiti.”
6 Ngakhale kuti anali kufunsira kwa Yehova,+ Yehova sanamuyankhe+ kaya kudzera m’maloto,+ Urimu+ kapena kudzera mwa aneneri.+