Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Munthu wosadetsedwayo awaze madziwo munthu wodetsedwayo pa tsiku lachitatu, ndi pa tsiku la 7. Ndipo pa tsiku la 7+ limenelo amuyeretse tchimo lake. Kenako amene akuyeretsedwayo achape zovala zake, asambe ndi madzi, ndipo akhale woyera madzulo ake.

  • Numeri 19:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “‘Koma munthu wodetsedwa akapanda kudziyeretsa, ameneyo aphedwe+ kuti asakhalenso pakati pa mpingowo, chifukwa waipitsa malo opatulika a Yehova. Iye sanawazidwe madzi oyeretsera. Choncho ndi wodetsedwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena